2 Samueli 18:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mlondayo nati, Ndiyesa kuti kuthamanga kwa wapatsogoloyo kunga kuthamanga kwa Ahimaazi mwana wa Zadoki, Ndipo mfumu inati, iye ndiye munthu wabwino, alikubwera ndi mau okoma.

2 Samueli 18

2 Samueli 18:25-28