2 Samueli 18:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mlondayo anaona munthu wina wothamanga; mlonda naitana wakucipata nanena, Taona munthu wina wakuthamanga yekha. Ndipo mfumu inati, iyenso abwera ndi mau.

2 Samueli 18

2 Samueli 18:21-33