2 Samueli 16:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kapena Yehova adzayang'anira cosayeneraci alikundicitira ine, ndipo Yehova adzandibwezera cabwino m'malo mwa kunditukwana kwa lero.

2 Samueli 16

2 Samueli 16:10-22