2 Samueli 16:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ananena ndi Abisai ndi anyamata ace onse, Onani, mwana wanga woturuka m'matumbo anga, alikufuna moyo wanga; koposa kotani nanga Mbenjamini uyu? mlekeni, atukwane, pakuti Yehova anamuuza.

2 Samueli 16

2 Samueli 16:3-20