2 Samueli 14:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inati, Apambukire ku nyumba yaiye yekha, koma asaone nkhope yanga. Comweco Abisalomu anapambukira ku nyumba ya iye yekha, wosaona nkhope ya mfumu.

2 Samueli 14

2 Samueli 14:19-27