2 Samueli 13:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco Amnoni anagona, nadzikokomeza alikudwala; ndipo pamene mfumu inadza kumuona, Amnoni anati kwa mfumuyo, Mulole Tamara mlongo wanga abwere ndi kundipangira timitanda tiwiri pamaso panga, kuti ndikadye ca m'manja mwace.

2 Samueli 13

2 Samueli 13:1-16