2 Samueli 13:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Abisalomu anathawa, nanka kwa Talimai mwana wa Amihuri mfumu ya ku Gesuri. Ndipo Davide analira mwana wace tsiku ndi tsiku.

2 Samueli 13

2 Samueli 13:29-39