2 Samueli 13:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Abisalomu anathawa. Ndipo mnyamata wakudikira anatukula maso ace nayang'ana, ndipo onani, m'mbuyo mwace anthu ambiri analikubwera m'njira yolambalala phiri.

2 Samueli 13

2 Samueli 13:29-39