2 Samueli 13:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tsono mfumu mbuye wanga asasauke mtima ndi cinthuci, ndi kuganiza kuti ana amuna onse a mfumu afa; pakuti Amnoni yekha wafa.

2 Samueli 13

2 Samueli 13:25-38