2 Samueli 13:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Amnoni anati kwa Tamara, Bwera naco cakudya kucipinda kuti ndikadye ca m'manja mwako. Ndipo Tamara anatenga timitanda anatipangato, nabwera nato kucipinda kwa Amnoni mlongo wace.

2 Samueli 13

2 Samueli 13:4-19