2 Samueli 13:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali citapita ici, popeza Abisalomu mwana wa Davide anali naye mlongo wace wokongola, dzina lace ndiye Tamara, Amnoni mwana wa Davide anamkonda iye.

2 Samueli 13

2 Samueli 13:1-10