2 Samueli 12:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndinakupatsa nyumba ya mbuye wako, ndi akazi a mbuye wako pa cifukato cako, ndinakupatsanso nyumba ya Israyeli ndi ya Yuda; ndipo zimenezi zikadakucepera ndikadakuonjezera zina zakuti zakuti.

2 Samueli 12

2 Samueli 12:1-9