2 Samueli 12:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Natani ananena kwa Davide, Munthuyo ndi inu nomwe. Atero Yehova, Mulungu wa Israyeli, Ndinakudzoza ukhale mfumu ya Israyeli, ndinakupulumutsa m'dzanja la Sauli;

2 Samueli 12

2 Samueli 12:1-10