2 Samueli 12:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, Taona ndidzakuutsira zoipa, zobadwa m'nyumba yako ya iwe wekha; ndipo ndidzacotsa akazi ako pamaso pako ndi kuwapatsa mnansi wako, amene adzagona ndi akazi ako dzuwa liri denene.

2 Samueli 12

2 Samueli 12:8-16