2 Samueli 12:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tsono lupanga silidzacoka pa nyumba yako nthawi zonse, popeza unandipeputsa Ine, nudzitengera mkazi wa Uriya Mhiti akhale mkazi wako.

2 Samueli 12

2 Samueli 12:2-17