2 Samueli 1:25-27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. Ha! amphamvuwo anagwa pakati pa nkhondo!Jonatani anaphedwa pamisanje pako.

26. Ndipsinjika mtima cifukwa ca iwe, mbale wanga Jonatani;Wandikomera kwambiri;Cikondi cako, ndinadabwa naco,Cinaposa cikondi ca anthu akazi.

27. Ha! amphamvuwo anagwa,Ndi zida za nkhondo zinaonengeka,

2 Samueli 1