2 Samueli 1:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipsinjika mtima cifukwa ca iwe, mbale wanga Jonatani;Wandikomera kwambiri;Cikondi cako, ndinadabwa naco,Cinaposa cikondi ca anthu akazi.

2 Samueli 1

2 Samueli 1:20-27