2 Samueli 1:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mapiri inu a Giliboa,Pa inu pasakhale mame kapena mvula, kapena minda yakutengako zopereka.Pakuti kumeneko zikopa za amphamvu zinatayika koipa,Cikopa ca Sauli, monga ca wosadzozedwa ndi mafuta.

2 Samueli 1

2 Samueli 1:12-22