2 Samueli 1:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usacinene ku Gati,Usacibukitse m'makwalala a Asikeloni,Kuti ana akazi a Afilisti angasekere,Kuti ana akazi a osadulidwawo angapfuule mokondwera.

2 Samueli 1

2 Samueli 1:10-25