2 Petro 3:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ambuye sazengereza nalo lonjezano, monga ena aciyesa cizengerezo; komatu aleza mtima kwa inu, wosafuna kuti ena aonongeke, koma kuti onse afike kukulapa.

2 Petro 3

2 Petro 3:8-18