2 Petro 3:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsiku la Ambuye lidzadza ngati mbala; m'mene miyamba idzapita ndi cibumo cacikuru, ndi zam'mwamba zidzakanganuka ndi kurentha kwakukuru, ndipo dziko ndi nchito ziri momwemo zidzarenthedwa.

2 Petro 3

2 Petro 3:1-12