2 Mbiri 9:30-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Ndipo Solomo anakhala mfumu ya Israyeli yense m'Yerusalemu zaka makumi anai.

31. Nagona Solomo pamodzi ndi makolo ace, naikidwa m'mudzi wa Davide atate wace; ndipo Rehabiamu mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

2 Mbiri 9