2 Mbiri 8:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Huramu anamtumizira zombo, ndi amarinyero ace, ndi anyamata akudziwa za m'nyanja; ndipo anamuka pamodzi ndi anyamata a Solomo ku Ofiri, natengako matalente mazana anai mphambu makumi asanu a golidi, nabwera nao kwa Solomo mfumu.

2 Mbiri 8

2 Mbiri 8:10-18