2 Mbiri 9:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo anali nazo zipinda zikwi zinai za akavalo ndi magareta, ndi apakavalo zikwi khumi ndi ziwiri; nawaika m'toidzi ya magareta, ndi m'Yerusalemu kwa mfumu.

2 Mbiri 9

2 Mbiri 9:16-28