2 Mbiri 4:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapanga zoikapo nyali khumi zagolidi, monga mwa ciweruzo cace; naziika m'Kacisi, zisanu ku dzanja lamanja, ndi zisanu ku dzanja lamanzere.

2 Mbiri 4

2 Mbiri 4:1-9