2 Mbiri 4:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anapanganso mbiya zamphwamphwa khumi, naika zisanu ku dzanja lamanja, ndi zisanu ku dzanja lamanzere, kutsukiramo; za nsembe yopsereza anazitsuka m'menemo; koma thawale ndi la ansembe kusambiramo.

2 Mbiri 4

2 Mbiri 4:1-13