2 Mbiri 36:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehoyakini anali wa zaka zisanu ndi zitatu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu miyezi itatu, ndi masiku khumi; nacita coipa pamaso pa Yehova.

2 Mbiri 36

2 Mbiri 36:8-10