2 Mbiri 36:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Macitidwe ena tsono a Yehoyakimu, ndi zonyansa zace anazicita, ndi zija zidapezeka zomtsutsa; taonani, zilembedwa m'buku la mafumu a Israyeli ndi Yuda; ndi Yehoyakini mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

2 Mbiri 36

2 Mbiri 36:3-17