2 Mbiri 36:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehoyakimu anali wa zaka makumi awiri mphambu zisanu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka khumi ndi cimodzi, nacita coipa pamaso pa Yehova Mulungu wace.

2 Mbiri 36

2 Mbiri 36:1-13