2 Mbiri 36:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mfumu ya Aigupto anamlonga Eliyakimu mng'ono wace mfumu ya Yuda ndi Yerusalemu, nasintha dzina lace likhale Yehoyakimu. Koma Neko anatenga Yehoahazi mkuru wace, namuka naye ku Aigupto.

2 Mbiri 36

2 Mbiri 36:3-6