2 Mbiri 35:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muimirire m'malo opatulika, monga mwa magawidwe a nyumba za makolo za abale anu ana a anthu, akhale nalo onse gawo la nyumba ya makolo ya Alevi.

2 Mbiri 35

2 Mbiri 35:1-10