2 Mbiri 35:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mudzikonzere monga mwa nyumba za makolo anu, m'zigawo zanu, monga umo adalembera Davide mfumu ya Israyeli, ndi umo adalembera Solomo mwana wace.

2 Mbiri 35

2 Mbiri 35:1-5