2 Mbiri 35:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaika ansembe pa udikiro wao, nawalimbikitsa acite utumiki wa nyumba ya Yehova.

2 Mbiri 35

2 Mbiri 35:1-10