2 Mbiri 35:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Yosiya anacitira Yehova Paskha m'Yerusalemu, naphera Paskha tsiku lakhumi ndi cinai la mwezi woyamba.

2 Mbiri 35

2 Mbiri 35:1-3