2 Mbiri 34:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

anazipereka kwa amisiri a mitengo ndi omanga nyumba, agule miyala yosema, ndi mitengo ya mitanda yam'mwamba ndi yammunsi ya nyumbazi, adaziononga mafumu a Yuda.

2 Mbiri 34

2 Mbiri 34:7-18