2 Mbiri 34:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anazipereka m'dzanja la anchito oikidwa ayang'anire nyumba ya Yehova; ndi iwo anazipereka kwa anchito akucita m'nyumba ya Yehova, kukonza ndi kulimbitsa nyumbayi;

2 Mbiri 34

2 Mbiri 34:7-13