2 Mbiri 33:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nacita coipa pamaso pa Yehova, monga mwa zonyansa za amitundu, amene Yehova anawacotsa m'dziko mwao pamaso pa ana a Israyeli.

2 Mbiri 33

2 Mbiri 33:1-12