2 Mbiri 33:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Manase anali wa zaka khumi ndi ziwiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi asanu mphambu zisanu.

2 Mbiri 33

2 Mbiri 33:1-9