2 Mbiri 31:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pobuka mau aja, ana a Israyeli anapereka mocuruka, zobala zoyamba za tirigu, vinyo, ndi mafuta, ndi uci, ndi za zipatso zonse za m'minda, ndi limodzi la magawo khumi la zonse anabwera nazo mocuruka.

2 Mbiri 31

2 Mbiri 31:1-13