2 Mbiri 30:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amtokoma anapitira m'midzi m'midzi mwa dziko la Efraimu ndi Manase, mpaka Zebuloni; koma anawaseka pwepwete nawanyodola.

2 Mbiri 30

2 Mbiri 30:5-15