2 Mbiri 29:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanena Hezekiya kuti apereke nsembe yopsereza pa guwa la nsembe. Ndipo pakuyamba nsembe yopsereza, inayambanso nyimbo ya Yehova ndi malipenga, pamodzi ndi zoyimbira za Davideyo mfumu ya Israyeli.

2 Mbiri 29

2 Mbiri 29:23-30