2 Mbiri 29:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Hezekiya analowa ufumu wace ali wa zaka makumi awiri mphambu zisanu, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zinai; ndi dzina la mace ndiye Abiya mwana wa Zekariya.

2 Mbiri 29

2 Mbiri 29:1-10