2 Mbiri 28:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi Ahazi anagona ndi makolo ace, namuika m'mudzi wa Yerusalemu; pakuti sanadza naye ku manda a mafumu a Israyeli; ndipo Hezekiya mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

2 Mbiri 28

2 Mbiri 28:19-27