2 Mbiri 26:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

popeza anaturuka, nayambana ndi Afilisti, nagamula linga la Gati, ndi linga la Yabine, ndi linga la Asidodi; namanga midzi m'dziko la Asidodi, ndi mwa Afilisti.

2 Mbiri 26

2 Mbiri 26:1-10