2 Mbiri 26:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anali munthu wakufuna Mulungu masiku a Zekariya, ndiye wozindikira masomphenya a Mulungu; ndipo masiku akufunira Yehova iye, Mulungu anamlemereza;

2 Mbiri 26

2 Mbiri 26:2-15