2 Mbiri 25:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma wosamvera Amaziya, pakuti nca Mulungu ici kuti awapereke m'dzanja la adani ao; popeza anafuna milungu ya Edomu.

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:19-22