2 Mbiri 25:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukuti, Taonani, ndakantha Aedomu, nukwezeka mtima wanu kudzikuza; khalani kwanu tsopano, mungadziutsire tsoka, mungagwe, inu, ndi Yuda pamodzi ndi inu.

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:15-23