2 Mbiri 23:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma asalowe mmodzi m'nyumba ya Yehova, ansembe okha, ndi Alevi otumikira, alowe iwowa; pakuti ndiwo opatulika; koma anthu onse asunge udikiro wa Yehova.

2 Mbiri 23

2 Mbiri 23:1-16