2 Mbiri 23:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anaturutsa mwana wa mfumu, nambveka korona, nampatsa mboni, namlonga ufumu; ndi Yehoyada ndi ana ace anamdzoza, nati, Ikhale ndi moyo mfumu.

2 Mbiri 23

2 Mbiri 23:10-15