2 Mbiri 23:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaika anthu onse, yense ndi cida cace m'dzanja lace, amzinge mfumu, kuyambira mbali ya ku dzanja lamanja la nyumba kufikira mbali ya ku dzanja lamanzere la nyumba, kuloza ku guwa la nsembe ndi kunyumba.

2 Mbiri 23

2 Mbiri 23:6-14